1 Yohane 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komatu ngati tikuyenda mʼkuwala mofanana ndi mmenenso iye alili mʼkuwala, ndiye kuti ndife ogwirizana ndipo magazi a Yesu, yemwe ndi Mwana wake, akutiyeretsa ku machimo onse.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, tsa. 27
7 Komatu ngati tikuyenda mʼkuwala mofanana ndi mmenenso iye alili mʼkuwala, ndiye kuti ndife ogwirizana ndipo magazi a Yesu, yemwe ndi Mwana wake, akutiyeretsa ku machimo onse.+