1 Yohane 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amene amakonda mʼbale wake ndiye kuti ali mʼkuwala+ ndipo palibe chimene chingachititse kuti apunthwe. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:10 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, tsa. 28
10 Amene amakonda mʼbale wake ndiye kuti ali mʼkuwala+ ndipo palibe chimene chingachititse kuti apunthwe.