1 Yohane 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikulembera inu abambo, chifukwa mukumudziwa amene wakhala alipo kuyambira pachiyambi. Ndikulemberanso inu anyamata chifukwa mwagonjetsa woipayo.+ Ndikulembera inu ana okondedwa chifukwa mukuwadziwa Atate.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:13 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, ptsa. 28-29
13 Ndikulembera inu abambo, chifukwa mukumudziwa amene wakhala alipo kuyambira pachiyambi. Ndikulemberanso inu anyamata chifukwa mwagonjetsa woipayo.+ Ndikulembera inu ana okondedwa chifukwa mukuwadziwa Atate.+