1 Yohane 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikulembera inu abambo chifukwa mukumudziwa iye amene wakhalapo kuyambira pachiyambi. Ndikulembera inu anyamata chifukwa ndinu olimba+ ndipo mumakhulupirira mawu a Mulungu+ komanso mwagonjetsa woipayo.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:14 Nsanja ya Olonda,2/1/2003, tsa. 81/15/1987, ptsa. 28-29
14 Ndikulembera inu abambo chifukwa mukumudziwa iye amene wakhalapo kuyambira pachiyambi. Ndikulembera inu anyamata chifukwa ndinu olimba+ ndipo mumakhulupirira mawu a Mulungu+ komanso mwagonjetsa woipayo.+