1 Yohane 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndakulemberani zimenezi, osati chifukwa chakuti simukudziwa choonadi+ koma chifukwa chakuti mukuchidziwa ndiponso chifukwa chakuti palibe bodza lililonse limene limachokera mʼchoonadi.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:21 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, tsa. 30
21 Ndakulemberani zimenezi, osati chifukwa chakuti simukudziwa choonadi+ koma chifukwa chakuti mukuchidziwa ndiponso chifukwa chakuti palibe bodza lililonse limene limachokera mʼchoonadi.+