1 Yohane 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taganizirani za chikondi chachikulu chimene Atate watisonyeza+ potitchula kuti ana ake.*+ Ndipo ndifedi ana ake. Nʼchifukwa chake dziko silikutidziwa,+ popeza iyeyo silikumudziwanso.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:1 Nsanja ya Olonda,9/15/2015, tsa. 182/1/1987, tsa. 8
3 Taganizirani za chikondi chachikulu chimene Atate watisonyeza+ potitchula kuti ana ake.*+ Ndipo ndifedi ana ake. Nʼchifukwa chake dziko silikutidziwa,+ popeza iyeyo silikumudziwanso.+