1 Yohane 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Okondedwa, tsopano ndife ana a Mulungu,+ koma panopa sizinaonekerebe kuti tidzakhala otani.+ Tikudziwa kuti akadzaonekera, tidzakhala ngati iyeyo, chifukwa tidzamuona mmene alili. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2020, ptsa. 8-9 Nsanja ya Olonda,12/15/2008, tsa. 272/1/1987, tsa. 8
2 Okondedwa, tsopano ndife ana a Mulungu,+ koma panopa sizinaonekerebe kuti tidzakhala otani.+ Tikudziwa kuti akadzaonekera, tidzakhala ngati iyeyo, chifukwa tidzamuona mmene alili.
3:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2020, ptsa. 8-9 Nsanja ya Olonda,12/15/2008, tsa. 272/1/1987, tsa. 8