1 Yohane 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense amene ali wogwirizana ndi Yesu sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo.+ Amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo ndiye kuti samukhulupirira* kapena kumudziwa. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,3/1/1991, tsa. 272/1/1987, tsa. 9
6 Aliyense amene ali wogwirizana ndi Yesu sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo.+ Amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo ndiye kuti samukhulupirira* kapena kumudziwa.