1 Yohane 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Mulungu ndiponso ana a Mdyerekezi tingawadziwe ndi mfundo iyi: Aliyense amene sachita zolungama ndiye kuti satsanzira Mulungu, chimodzimodzinso amene sakonda mʼbale wake.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:10 Nsanja ya Olonda,2/1/1987, ptsa. 9-10
10 Ana a Mulungu ndiponso ana a Mdyerekezi tingawadziwe ndi mfundo iyi: Aliyense amene sachita zolungama ndiye kuti satsanzira Mulungu, chimodzimodzinso amene sakonda mʼbale wake.+