1 Yohane 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tisakhale ngati Kaini, amene ankatsanzira woipayo ndipo anapha mʼbale wake.+ Nʼchifukwa chiyani anapha mʼbale wake? Chifukwa chakuti zochita zake zinali zoipa,+ koma za mʼbale wake zinali zolungama.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:12 Mphunzitsi Waluso, tsa. 225 Nsanja ya Olonda,2/1/1987, ptsa. 9-10
12 Tisakhale ngati Kaini, amene ankatsanzira woipayo ndipo anapha mʼbale wake.+ Nʼchifukwa chiyani anapha mʼbale wake? Chifukwa chakuti zochita zake zinali zoipa,+ koma za mʼbale wake zinali zolungama.+