1 Yohane 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tikudziwa kuti tinali ngati akufa koma tsopano ndife amoyo+ chifukwa timakonda abale athu.+ Amene sakonda mʼbale wake ndiye kuti adakali wakufa.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Nsanja ya Olonda,2/1/1987, tsa. 10
14 Tikudziwa kuti tinali ngati akufa koma tsopano ndife amoyo+ chifukwa timakonda abale athu.+ Amene sakonda mʼbale wake ndiye kuti adakali wakufa.+