1 Yohane 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Aliyense amene ali ndi zinthu zofunika pa moyo ndipo akuona mʼbale wake akuvutika chifukwa chosowa zinthuzo, koma osamusonyeza chifundo, kodi tingati munthu ameneyu amakonda Mulungu?+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:17 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2020, tsa. 24 Nsanja ya Olonda,10/1/1997, tsa. 32
17 Aliyense amene ali ndi zinthu zofunika pa moyo ndipo akuona mʼbale wake akuvutika chifukwa chosowa zinthuzo, koma osamusonyeza chifundo, kodi tingati munthu ameneyu amakonda Mulungu?+