1 Yohane 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Lamulo limene anatipatsa ndi lakuti, tikhale ndi chikhulupiriro mʼdzina la Mwana wake Yesu Khristu+ ndiponso tizikondana,+ monga mmene iye anatilamulira. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:23 Nsanja ya Olonda,2/1/1987, tsa. 11
23 Lamulo limene anatipatsa ndi lakuti, tikhale ndi chikhulupiriro mʼdzina la Mwana wake Yesu Khristu+ ndiponso tizikondana,+ monga mmene iye anatilamulira.