1 Yohane 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mantha amatichititsa kukhala omangika. Koma munthu amene amakonda Mulungu sachita mantha,+ chifukwa chikondi chimene chili chokwanira chimathetsa mantha. Munthu amene amachita mantha, chikondi chake si chokwanira.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:18 Nsanja ya Olonda,10/1/2004, tsa. 298/1/1995, tsa. 312/1/1987, ptsa. 15-16
18 Mantha amatichititsa kukhala omangika. Koma munthu amene amakonda Mulungu sachita mantha,+ chifukwa chikondi chimene chili chokwanira chimathetsa mantha. Munthu amene amachita mantha, chikondi chake si chokwanira.+