1 Yohane 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso, popeza timadziwa kuti amatimvera tikapempha chilichonse, timakhala ndi chikhulupiriro kuti tilandira zinthu zimene tamupemphazo.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:15 Nsanja ya Olonda,2/1/1987, tsa. 17
15 Komanso, popeza timadziwa kuti amatimvera tikapempha chilichonse, timakhala ndi chikhulupiriro kuti tilandira zinthu zimene tamupemphazo.+