1 Yohane 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tikudziwa kuti munthu aliyense yemwe ndi mwana wa Mulungu alibe chizolowezi chochita tchimo, koma mwana* wa Mulungu amamuyangʼanira ndipo woipayo sangamugwire.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:18 Nsanja ya Olonda,2/1/1987, tsa. 18
18 Tikudziwa kuti munthu aliyense yemwe ndi mwana wa Mulungu alibe chizolowezi chochita tchimo, koma mwana* wa Mulungu amamuyangʼanira ndipo woipayo sangamugwire.+