2 Yohane 1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine monga munthu wachikulire,* ndikulembera mayi wosankhidwa ndi Mulungu ndiponso ana ake amene ndimawakonda kwambiri. Ndipo si ine ndekha amene ndimawakonda, chifukwa onse amene adziwa choonadi amawakondanso. 2 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1 Nsanja ya Olonda,12/15/2008, tsa. 28 Galamukani!,11/8/1998, tsa. 20
1 Ine monga munthu wachikulire,* ndikulembera mayi wosankhidwa ndi Mulungu ndiponso ana ake amene ndimawakonda kwambiri. Ndipo si ine ndekha amene ndimawakonda, chifukwa onse amene adziwa choonadi amawakondanso.