2 Yohane 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komabe samalani chifukwa anthu ambiri opusitsa anzawo ayamba kupezeka mʼdzikoli.+ Anthu amenewa amatsutsa zoti Yesu Khristu anabwera monga munthu.+ Amene amachita zimenezi ndi wopusitsa ena ndiponso wokana Khristu.+ 2 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,6/1/2015, tsa. 1412/15/2008, tsa. 28
7 Komabe samalani chifukwa anthu ambiri opusitsa anzawo ayamba kupezeka mʼdzikoli.+ Anthu amenewa amatsutsa zoti Yesu Khristu anabwera monga munthu.+ Amene amachita zimenezi ndi wopusitsa ena ndiponso wokana Khristu.+