2 Yohane 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Samalani kuti musataye zinthu zimene tinakuthandizani kuti muzipeze nʼcholinga choti mudzalandire madalitso onse amene Mulungu wakukonzerani.+ 2 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8 Nsanja ya Olonda,2/1/1988, tsa. 30
8 Samalani kuti musataye zinthu zimene tinakuthandizani kuti muzipeze nʼcholinga choti mudzalandire madalitso onse amene Mulungu wakukonzerani.+