2 Yohane 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense amene amachita zosemphana ndi zimene Khristu ankaphunzitsa, ndiye kuti akukana Mulungu.+ Koma Atate ndiponso Mwana, amasangalala ndi munthu amene amachita zinthu mogwirizana ndi zimene iye ankaphunzitsa.+ 2 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 57
9 Aliyense amene amachita zosemphana ndi zimene Khristu ankaphunzitsa, ndiye kuti akukana Mulungu.+ Koma Atate ndiponso Mwana, amasangalala ndi munthu amene amachita zinthu mogwirizana ndi zimene iye ankaphunzitsa.+