-
2 Yohane 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ngakhale kuti ndili ndi zambiri zoti ndikulembereni, sindikufuna kuzilemba papepala ndi inki. Koma ndikuyembekezera kubwera kwa inu kuti ndidzalankhule nanu pamasomʼpamaso nʼcholinga choti mudzasangalale kwambiri.
-