-
3 Yohane 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma ndikuganiza kuti tionana posachedwapa ndipo tidzalankhulana pamasomʼpamaso.
Mtendere ukhale nawe.
Abale kuno akukupatsa moni. Iwenso undiperekere moni kwa abale kumeneko, aliyense payekhapayekha.
-