Yuda 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale zili choncho, anthu amene alowa mozembawa nawonso amakonda zongolota, amaipitsa matupi awo komanso a ena,* amanyoza ulamuliro ndiponso amanenera zamwano anthu amene Mulungu wawapatsa ulemerero.+ Yuda Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8 Nsanja ya Olonda,10/15/2012, tsa. 136/1/1998, ptsa. 16-179/1/1997, tsa. 16
8 Ngakhale zili choncho, anthu amene alowa mozembawa nawonso amakonda zongolota, amaipitsa matupi awo komanso a ena,* amanyoza ulamuliro ndiponso amanenera zamwano anthu amene Mulungu wawapatsa ulemerero.+