Yuda 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ali ngatinso mafunde oopsa apanyanja otulutsa thovu la zinthu zowachititsa manyazi,+ ndiponso nyenyezi zoyenda mopanda dongosolo, ndipo Mulungu wawaika mumdima wandiweyani mmene adzakhalemo mpaka kalekale.+
13 Ali ngatinso mafunde oopsa apanyanja otulutsa thovu la zinthu zowachititsa manyazi,+ ndiponso nyenyezi zoyenda mopanda dongosolo, ndipo Mulungu wawaika mumdima wandiweyani mmene adzakhalemo mpaka kalekale.+