Yuda 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Apulumutseni+ powachotsa mofulumira pamoto. Pitirizaninso kuchitira chifundo anthu ena, koma muzisamala. Powachitira chifundocho, muzidana ndi zovala zawo zomwe azidetsa ndi makhalidwe oipa.*+ Yuda Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 21
23 Apulumutseni+ powachotsa mofulumira pamoto. Pitirizaninso kuchitira chifundo anthu ena, koma muzisamala. Powachitira chifundocho, muzidana ndi zovala zawo zomwe azidetsa ndi makhalidwe oipa.*+