Yuda 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu wathu waulemerero angathe kukutetezani kuti musagwe ndiponso kukuthandizani kuti muime pamaso pake opanda cholakwa+ mukusangalala kwambiri. Yuda Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24 Nsanja ya Olonda,3/15/2012, ptsa. 21-22
24 Mulungu wathu waulemerero angathe kukutetezani kuti musagwe ndiponso kukuthandizani kuti muime pamaso pake opanda cholakwa+ mukusangalala kwambiri.