Chivumbulutso 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakati pa zoikapo nyalezo, panali wina wooneka ngati mwana wa munthu+ atavala chovala chofika kumapazi ndipo anali atamanga lamba wagolide pachifuwa. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:13 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 25
13 Pakati pa zoikapo nyalezo, panali wina wooneka ngati mwana wa munthu+ atavala chovala chofika kumapazi ndipo anali atamanga lamba wagolide pachifuwa.