Chivumbulutso 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mapazi ake anali ngati kopa* woyengedwa bwino+ amene akunyezimira mʼngʼanjo ndipo mawu ake ankamveka ngati mkokomo wa madzi ambiri. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:15 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 25-26
15 Mapazi ake anali ngati kopa* woyengedwa bwino+ amene akunyezimira mʼngʼanjo ndipo mawu ake ankamveka ngati mkokomo wa madzi ambiri.