Chivumbulutso 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mʼdzanja lake lamanja anali ndi nyenyezi 7.+ Mʼkamwa mwake munkatuluka lupanga lalitali, lakuthwa konsekonse.+ Nkhope yake inali yowala ngati dzuwa limene likuwala kwambiri.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:16 Nsanja ya Olonda,10/15/2012, tsa. 14 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 26-27, 28-29
16 Mʼdzanja lake lamanja anali ndi nyenyezi 7.+ Mʼkamwa mwake munkatuluka lupanga lalitali, lakuthwa konsekonse.+ Nkhope yake inali yowala ngati dzuwa limene likuwala kwambiri.+