Chivumbulutso 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amene ali ndi makutu amve zimene mzimu ukunena ku mipingo kuti:+ Amene wapambana pankhondo,+ ndidzamulola kudya zipatso zamumtengo wa moyo+ umene uli mʼparadaiso wa Mulungu.’ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:7 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 315/15/2003, tsa. 11 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 36-37, 306
7 Amene ali ndi makutu amve zimene mzimu ukunena ku mipingo kuti:+ Amene wapambana pankhondo,+ ndidzamulola kudya zipatso zamumtengo wa moyo+ umene uli mʼparadaiso wa Mulungu.’