Chivumbulutso 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Pegamo lemba kuti: Izi ndi zimene akunena amene ali ndi lupanga lalitali, lakuthwa konsekonse:+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:12 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 41-42 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 13
12 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Pegamo lemba kuti: Izi ndi zimene akunena amene ali ndi lupanga lalitali, lakuthwa konsekonse:+