Chivumbulutso 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuwonjezera pamenepo, ulinso ndi anthu amene akupitiriza kutsatira chiphunzitso cha mpatuko wa Nikolao.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:15 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 30, 44-45 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 144/1/1989, tsa. 12
15 Kuwonjezera pamenepo, ulinso ndi anthu amene akupitiriza kutsatira chiphunzitso cha mpatuko wa Nikolao.+