Chivumbulutso 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ulape. Ngati sulapa, ndibwera kwa iwe mwamsanga, ndipo ndidzamenyana nawo ndi lupanga lalitali lamʼkamwa mwanga.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:16 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 31-32, 44-45 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 14
16 Choncho ulape. Ngati sulapa, ndibwera kwa iwe mwamsanga, ndipo ndidzamenyana nawo ndi lupanga lalitali lamʼkamwa mwanga.+