-
Chivumbulutso 2:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 ‘Ndikudziwa ntchito zako, chikondi chako, chikhulupiriro chako, utumiki wako komanso kupirira kwako. Ndikudziwanso kuti ntchito zako zapanopa nʼzambiri kuposa zimene unkachita poyamba.
-