Chivumbulutso 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komabe, ndakupeza ndi mlandu wakuti ukulekerera mayi uja Yezebeli,+ amene amadziona ngati mneneri. Iye akuphunzitsa ndi kusocheretsa akapolo anga kuti azichita chiwerewere*+ komanso kuti azidya zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:20 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 30, 48-49 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 164/1/1990, tsa. 304/1/1989, tsa. 13
20 Komabe, ndakupeza ndi mlandu wakuti ukulekerera mayi uja Yezebeli,+ amene amadziona ngati mneneri. Iye akuphunzitsa ndi kusocheretsa akapolo anga kuti azichita chiwerewere*+ komanso kuti azidya zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano.
2:20 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 30, 48-49 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 164/1/1990, tsa. 304/1/1989, tsa. 13