Chivumbulutso 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ulamuliro wake udzakhala wofanana ndi umene ine ndalandira kuchokera kwa Atate wanga. Iye adzakusa anthu ndi ndodo yachitsulo+ moti anthuwo adzaphwanyidwaphwanyidwa ngati mbiya zadothi. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:27 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 53, 281 Nsanja ya Olonda,8/15/1990, tsa. 31
27 Ulamuliro wake udzakhala wofanana ndi umene ine ndalandira kuchokera kwa Atate wanga. Iye adzakusa anthu ndi ndodo yachitsulo+ moti anthuwo adzaphwanyidwaphwanyidwa ngati mbiya zadothi.