Chivumbulutso 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Filadefiya lemba kuti: Izi ndi zimene akunena woyerayo,+ amene ndi woona,+ yemwe ali ndi kiyi wa Davide.+ Iye amene amati akatsegula palibe amene angatseke, ndipo akatseka palibe amene angatsegule. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:7 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 315/15/2003, tsa. 17 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 58-60, 63
7 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Filadefiya lemba kuti: Izi ndi zimene akunena woyerayo,+ amene ndi woona,+ yemwe ali ndi kiyi wa Davide.+ Iye amene amati akatsegula palibe amene angatseke, ndipo akatseka palibe amene angatsegule.