Chivumbulutso 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taona! Anthu ochokera mʼsunagoge wa Satana, amene amanama kuti ndi Ayuda pamene si Ayuda,+ ndidzawachititsa kuti abwere kudzagwada nʼkuwerama pamapazi ako. Ndipo ndidzawachititsa kuti adziwe kuti ndimakukonda. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 60-62, 63-64
9 Taona! Anthu ochokera mʼsunagoge wa Satana, amene amanama kuti ndi Ayuda pamene si Ayuda,+ ndidzawachititsa kuti abwere kudzagwada nʼkuwerama pamapazi ako. Ndipo ndidzawachititsa kuti adziwe kuti ndimakukonda.