-
Chivumbulutso 3:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Taona! Ndaima pakhomo ndipo ndikugogoda. Wina akamva mawu anga nʼkutsegula chitseko, ndidzalowa mʼnyumba mwake ndipo iye ndi ine tidzadyera limodzi chakudya chamadzulo.
-