Chivumbulutso 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kumpando wachifumuko kunkatuluka mphezi,+ mawu komanso mabingu.+ Panalinso nyale zamoto 7 zimene zinkayaka patsogolo pa mpando wachifumuwo. Nyalezo zikuimira mizimu 7 ya Mulungu.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:5 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 30 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 77-79
5 Kumpando wachifumuko kunkatuluka mphezi,+ mawu komanso mabingu.+ Panalinso nyale zamoto 7 zimene zinkayaka patsogolo pa mpando wachifumuwo. Nyalezo zikuimira mizimu 7 ya Mulungu.+