-
Chivumbulutso 5:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndipo ndinaona mngelo wamphamvu akulengeza ndi mawu okweza kuti: “Ndi ndani ali woyenera kumatula zidindo zimene amatira mpukutuwu nʼkuutsegula?”
-