Chivumbulutso 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atamatula chidindo cha 5, ndinaona pansi pa guwa lansembe+ pali miyoyo*+ ya anthu amene anaphedwa chifukwa cha mawu a Mulungu ndiponso chifukwa cha ntchito yochitira umboni.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:9 Nsanja ya Olonda,1/1/2007, ptsa. 28-29 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 100, 289
9 Atamatula chidindo cha 5, ndinaona pansi pa guwa lansembe+ pali miyoyo*+ ya anthu amene anaphedwa chifukwa cha mawu a Mulungu ndiponso chifukwa cha ntchito yochitira umboni.+