11 Aliyense wa iwo anapatsidwa mkanjo woyera+ ndipo anauzidwa kuti apumulebe kanthawi pangʼono, mpaka chiwerengero cha akapolo anzawo chitakwanira, inde chiwerengero cha abale awo amene anali atatsala pangʼono kuphedwa ngati mmenenso iwowo anaphedwera.+