Chivumbulutso 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atamatula chidindo cha 6, ndinaona kuti kunachitika chivomerezi chachikulu. Dzuwa linada ngati chiguduli choluka ndi ubweya* ndipo mwezi wonse unafiira ngati magazi.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:12 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 104-110 Nsanja ya Olonda,10/15/1988, tsa. 17
12 Atamatula chidindo cha 6, ndinaona kuti kunachitika chivomerezi chachikulu. Dzuwa linada ngati chiguduli choluka ndi ubweya* ndipo mwezi wonse unafiira ngati magazi.+