-
Chivumbulutso 6:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Nyenyezi zakumwamba zinagwera padziko lapansi ngati mmene mtengo wa mkuyu umene ukugwedezeka ndi mphepo yamphamvu umagwetsera nkhuyu zake zosapsa.
-