Chivumbulutso 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mngelo wina anafika atanyamula chiwiya chofukizira chagolide nʼkuima paguwa lansembe.+ Iye anapatsidwa zofukiza zambiri+ kuti azipereke nsembe limodzi ndi mapemphero a oyera onse paguwa lansembe lagolide,+ limene linali pamaso pa mpando wachifumu. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 129-131
3 Mngelo wina anafika atanyamula chiwiya chofukizira chagolide nʼkuima paguwa lansembe.+ Iye anapatsidwa zofukiza zambiri+ kuti azipereke nsembe limodzi ndi mapemphero a oyera onse paguwa lansembe lagolide,+ limene linali pamaso pa mpando wachifumu.