Chivumbulutso 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Utsi wa zofukizazo unakwera pamaso pa Mulungu kuchokera mʼdzanja la mngeloyo limodzi ndi mapemphero+ a oyera. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:4 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 129-131
4 Utsi wa zofukizazo unakwera pamaso pa Mulungu kuchokera mʼdzanja la mngeloyo limodzi ndi mapemphero+ a oyera.