Chivumbulutso 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma nthawi yomweyo, mngeloyo anatenga chiwiya chofukizira chija nʼkudzazitsamo moto umene anapala paguwa lansembe nʼkuuponyera padziko lapansi. Ndiyeno kunagunda mabingu, kunamveka mawu, kunachita mphezi+ komanso chivomerezi. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:5 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 32 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 131
5 Koma nthawi yomweyo, mngeloyo anatenga chiwiya chofukizira chija nʼkudzazitsamo moto umene anapala paguwa lansembe nʼkuuponyera padziko lapansi. Ndiyeno kunagunda mabingu, kunamveka mawu, kunachita mphezi+ komanso chivomerezi.