Chivumbulutso 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Angelo 7 amene anali ndi malipenga 7 aja, anakonzekera kuliza malipengawo.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:6 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 132