Chivumbulutso 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mngelo wachitatu analiza lipenga lake. Ndipo nyenyezi yaikulu imene inkayaka ngati nyale inagwa kuchokera kumwamba. Inagwera pagawo limodzi mwa magawo atatu a mitsinje, ndi pa akasupe a madzi.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:10 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 136-138 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 12
10 Mngelo wachitatu analiza lipenga lake. Ndipo nyenyezi yaikulu imene inkayaka ngati nyale inagwa kuchokera kumwamba. Inagwera pagawo limodzi mwa magawo atatu a mitsinje, ndi pa akasupe a madzi.+